Levitiko 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Ili ndi lamulo la nsembe yamachimo:+ Pamalo amene mukuphera nyama ya nsembe yopsereza+ muzipheraponso nyama ya nsembe yamachimo pamaso pa Yehova. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.
25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Ili ndi lamulo la nsembe yamachimo:+ Pamalo amene mukuphera nyama ya nsembe yopsereza+ muzipheraponso nyama ya nsembe yamachimo pamaso pa Yehova. Nsembeyi ndi yopatulika koposa.