Levitiko 6:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yamachimo+ lili motere: Nyama ya nsembe yamachimo iziphedwa pamaso pa Yehova, pamalo+ ophera nyama ya nsembe yopsereza nthawi zonse. Chimenechi ndi chinthu chopatulika koposa.+
25 “Uza Aroni ndi ana ake kuti, ‘Lamulo la nsembe yamachimo+ lili motere: Nyama ya nsembe yamachimo iziphedwa pamaso pa Yehova, pamalo+ ophera nyama ya nsembe yopsereza nthawi zonse. Chimenechi ndi chinthu chopatulika koposa.+