Levitiko 21:22 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 22 Iye angadye mkate wa Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+ Levitiko 22:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Dzuwa likalowa akhalenso woyera, ndipo pambuyo pake akhoza kudya zina mwa zinthu zopatulika, chifukwa ndi chakudya chake.+
22 Iye angadye mkate wa Mulungu wake kuchokera pa zinthu zopatulika koposa+ ndi pa zinthu zopatulika.+
7 Dzuwa likalowa akhalenso woyera, ndipo pambuyo pake akhoza kudya zina mwa zinthu zopatulika, chifukwa ndi chakudya chake.+