Levitiko 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma nyama ya nsembe yamachimo sikuyenera kudyedwa ngati ena mwa magazi ake analowa nawo mʼchihema chokumanako kuti aphimbire machimo mʼmalo oyera.+ Imeneyo muziiwotcha pamoto.’”
30 Koma nyama ya nsembe yamachimo sikuyenera kudyedwa ngati ena mwa magazi ake analowa nawo mʼchihema chokumanako kuti aphimbire machimo mʼmalo oyera.+ Imeneyo muziiwotcha pamoto.’”