Levitiko 6:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto.
30 Koma musadye nyama ya nsembe yamachimo imene ena mwa magazi+ ake adzalowa nawo m’chihema chokumanako kuti aphimbire machimo m’malo oyerawo. Imeneyo muziitentha ndi moto.