Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Levitiko 4:5
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Pamenepo wansembe, wodzozedwayo,+ azitengako pang’ono magazi a ng’ombeyo ndi kulowa nawo m’chihema chokumanako.

  • Levitiko 10:18
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 18 Taonani, simunabweretse magazi ake mkati, m’malo oyera.+ Munafunika kudya nsembeyo m’malo oyera, monga mmene Mulungu anandilamulira.”+

  • Levitiko 16:27
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 27 “Koma ng’ombe yamphongo ya nsembe yamachimo ndi mbuzi ya nsembe yamachimo zimene magazi ake analowa nawo m’malo oyera pokaphimba machimo, azizitulutsira kunja kwa msasa ndipo azitentha pamoto zikopa zake, nyama ndi ndowe zake.+

  • Aheberi 13:11
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 11 Pakuti nyama zimene magazi ake, mkulu wa ansembe amalowa nawo m’malo oyera chifukwa cha machimo, amakazitentha kunja kwa msasa.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena