Levitiko 8:7 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ nʼkumumanga lamba wapamimba.*+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi+ ndipo anamanga lamba woluka+ wa efodiyo.
7 Atatero anaveka Aroni mkanjo+ nʼkumumanga lamba wapamimba.*+ Anamuvekanso malaya odula manja+ komanso efodi+ ndipo anamanga lamba woluka+ wa efodiyo.