Levitiko 13:2 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 2 “Munthu akatuluka chotupa, kapena nkhanambo,* kapena chikanga, moti ingathe kukhala nthenda ya khate*+ pakhungu lake, azibwera naye kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake omwenso ndi ansembe.+
2 “Munthu akatuluka chotupa, kapena nkhanambo,* kapena chikanga, moti ingathe kukhala nthenda ya khate*+ pakhungu lake, azibwera naye kwa Aroni wansembe, kapena kwa mmodzi wa ana ake omwenso ndi ansembe.+