-
Levitiko 14:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Wansembe adzalamula kuti atulutse katundu mʼnyumbamo iye asanafike kudzaona nthendayo. Adzachite zimenezi kuti wansembe asadzagamule kuti chilichonse mʼnyumbamo nʼchodetsedwa. Kenako wansembe adzabwere kudzaona nyumbayo.
-