-
Levitiko 14:36Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
36 Pamenepo wansembe azilamula kuti atulutse katundu m’nyumbamo iye asanafike kudzaona nthendayo. Azichita zimenezi kuti wansembe asagamule kuti chilichonse m’nyumbamo n’chodetsedwa. Akatero wansembe azibwera kudzaona nyumbayo.
-