Levitiko 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chilichonse chimene angagonepo pamene ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba chizikhala chodetsedwa, ndiponso chilichonse chimene wakhalapo chizikhala chodetsedwa.+
20 Chilichonse chimene angagonepo pamene ali wodetsedwa chifukwa chakuti akusamba chizikhala chodetsedwa, ndiponso chilichonse chimene wakhalapo chizikhala chodetsedwa.+