Levitiko 15:20 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 20 Chilichonse chimene angagonepo pamene ali wodetsedwa chifukwa cha kusamba kwake chizikhala chodetsedwa,+ ndiponso chilichonse chimene wakhalapo chizikhala chodetsedwa.
20 Chilichonse chimene angagonepo pamene ali wodetsedwa chifukwa cha kusamba kwake chizikhala chodetsedwa,+ ndiponso chilichonse chimene wakhalapo chizikhala chodetsedwa.