Levitiko 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 Polowa mʼmalo oyera, Aroni azitenga zotsatirazi: ngʼombe yaingʼono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+
3 Polowa mʼmalo oyera, Aroni azitenga zotsatirazi: ngʼombe yaingʼono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+