Levitiko 16:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “Polowa m’malo oyera,+ Aroni azitenga zotsatirazi: ng’ombe yaing’ono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+
3 “Polowa m’malo oyera,+ Aroni azitenga zotsatirazi: ng’ombe yaing’ono yamphongo kuti ikhale nsembe yamachimo,+ ndi nkhosa yamphongo kuti ikhale nsembe yopsereza.+