Levitiko 1:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako. Levitiko 8:18 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 18 Kenako anatenga nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.+
3 “‘Ngati akupereka ng’ombe kuti ikhale nsembe yake yopsereza,+ azipereka yamphongo, yopanda chilema.+ Aziipereka kwa Yehova mwa kufuna kwake,+ pakhomo la chihema chokumanako.
18 Kenako anatenga nkhosa yamphongo ya nsembe yopsereza, ndipo Aroni ndi ana ake anaika manja awo pamutu pa nkhosayo.+