Levitiko 16:17 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 17 Mʼchihema chokumanako musamapezeke munthu wina aliyense kuyambira nthawi imene Aroni walowa mʼmalo oyera kukaphimba machimo mpaka kutulukamo. Ndipo aziphimba machimo ake, a banja lake+ ndi a mpingo wonse wa Isiraeli.+
17 Mʼchihema chokumanako musamapezeke munthu wina aliyense kuyambira nthawi imene Aroni walowa mʼmalo oyera kukaphimba machimo mpaka kutulukamo. Ndipo aziphimba machimo ake, a banja lake+ ndi a mpingo wonse wa Isiraeli.+