Levitiko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Akatero Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake+ ndi a banja lake.*
6 Akatero Aroni azibweretsa ngʼombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo, ndipo aziphimba machimo ake+ ndi a banja lake.*