Levitiko 16:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 “Ndiponso Aroni azitenga ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo,+ ndipo aziphimba machimo+ ake+ ndi a nyumba yake.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 16:6 Nsanja ya Olonda,2/15/1998, tsa. 123/1/1987, tsa. 31
6 “Ndiponso Aroni azitenga ng’ombe yamphongo ya nsembe yake yamachimo,+ ndipo aziphimba machimo+ ake+ ndi a nyumba yake.+