Ekisodo 30:30 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 30 Udzoze Aroni+ ndi ana ake,+ ndipo uwayeretse kuti atumikire monga ansembe anga.+ Salimo 135:19 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 19 Inu nyumba ya Isiraeli, tamandani Yehova.+Inu nyumba ya Aroni, tamandani Yehova.+