Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • Aheberi 5:1-3
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 5 Mkulu wa ansembe aliyense wotengedwa pakati pa anthu, amaikidwa kuti azigwira ntchito ya Mulungu mʼmalo mwa anthu,+ kuti azipereka mphatso ndi nsembe zophimba machimo.+ 2 Amakhala woleza mtima pochita zinthu ndi anthu osadziwa kanthu komanso olakwa,* chifukwa iyenso ali ndi zofooka. 3 Ndipo chifukwa cha zimenezo, amafunika kupereka nsembe za machimo ake, ngati mmenenso amaperekera nsembe za machimo a anthu ena.+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena