Aheberi 5:1 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Mkulu wa ansembe aliyense wotengedwa mwa anthu amaikidwa kuti achite utumiki wa Mulungu m’malo mwa anthu,+ kuti azipereka mphatso ndi nsembe zophimba machimo.+ Aheberi Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 5:1 Nsanja ya Olonda,1/15/2012, tsa. 278/15/2000, tsa. 14
5 Mkulu wa ansembe aliyense wotengedwa mwa anthu amaikidwa kuti achite utumiki wa Mulungu m’malo mwa anthu,+ kuti azipereka mphatso ndi nsembe zophimba machimo.+