Levitiko 17:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 koma osabwera nayo pakhomo la chihema chokumanako kuti aipereke kwa Yehova, ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.+
9 koma osabwera nayo pakhomo la chihema chokumanako kuti aipereke kwa Yehova, ayenera kuphedwa kuti asakhalenso pakati pa anthu a mtundu wake.+