Levitiko 19:6 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 6 Muzidya nyama yoperekedwa nsembeyo pa tsiku limene mwaipereka ndiponso tsiku lotsatira, koma yotsala mpaka tsiku lachitatu muziiwotcha pamoto.+
6 Muzidya nyama yoperekedwa nsembeyo pa tsiku limene mwaipereka ndiponso tsiku lotsatira, koma yotsala mpaka tsiku lachitatu muziiwotcha pamoto.+