Levitiko 19:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+ Levitiko Buku Lofufuzira Nkhani la Mboni za Yehova la 2019 19:13 Nsanja ya Olonda (Yophunzira),12/2021, tsa. 10
13 Musamabere anzanu mwachinyengo+ ndipo musamalande zinthu za aliyense.+ Malipiro a munthu waganyu asagone mʼnyumba mwanu mpaka mʼmawa.+