-
Levitiko 23:14Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
14 Musamadye mkate, mbewu zokazinga kapena mbewu zatsopano mpaka tsiku limeneli litafika komanso mutabweretsa nsembe ya Mulungu wanu. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.
-