Levitiko 23:14 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 14 Musadye mkate, mbewu zokazinga kapena mbewu zatsopano kufikira tsiku limeneli,+ mpaka mutabweretsa nsembe ya Mulungu wanu. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.
14 Musadye mkate, mbewu zokazinga kapena mbewu zatsopano kufikira tsiku limeneli,+ mpaka mutabweretsa nsembe ya Mulungu wanu. Limeneli ndi lamulo mpaka kalekale ku mibadwo yanu yonse, kulikonse kumene mungakhale.