Levitiko 23:36 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.
36 Kwa masiku 7 muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Pa tsiku la 8 muzichita msonkhano wopatulika,+ ndipo muzipereka nsembe yowotcha pamoto kwa Yehova. Umenewu ndi msonkhano wapadera. Musamagwire ntchito iliyonse yotopetsa.