Levitiko 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ndipo ngati munthu amene akuperekedwayo ndi wamwamuna, wazaka zapakati pa 20 ndi 60, mtengo wake womwe unaikidwa ndi masekeli* asiliva 50, pamuyezo wofanana ndi sekeli yakumalo oyera.*
3 ndipo ngati munthu amene akuperekedwayo ndi wamwamuna, wazaka zapakati pa 20 ndi 60, mtengo wake womwe unaikidwa ndi masekeli* asiliva 50, pamuyezo wofanana ndi sekeli yakumalo oyera.*