Levitiko 27:3 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 3 ngati munthu woperekedwayo ndi wamwamuna, wazaka zapakati pa 20 ndi 60, mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva 50, pamuyezo wolingana ndi sekeli la kumalo oyera.*
3 ngati munthu woperekedwayo ndi wamwamuna, wazaka zapakati pa 20 ndi 60, mtengo wake woikidwiratu ndi masekeli asiliva 50, pamuyezo wolingana ndi sekeli la kumalo oyera.*