-
Levitiko 27:15Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
15 Koma amene wapereka nyumbayo akafuna kuiwombola, azipereka mtengo wa nyumbayo womwe unaikidwa nʼkuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo. Akatero nyumbayo izikhala yake.
-