Levitiko 27:15 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 15 Koma wopereka nyumbayo akafuna kuiwombola, azipereka mtengo woikidwiratu wa nyumbayo ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo asanu a mtengowo.+ Akatero azitenganso nyumbayo kukhala yake.
15 Koma wopereka nyumbayo akafuna kuiwombola, azipereka mtengo woikidwiratu wa nyumbayo ndi kuwonjezerapo gawo limodzi mwa magawo asanu a mtengowo.+ Akatero azitenganso nyumbayo kukhala yake.