Levitiko 27:27 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 27 Koma ngati ndi nyama yodetsedwa ndipo waiwombola mogwirizana ndi mtengo womwe unaikidwa, azipereka mtengo wa nyamayo nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+ Koma ngati sangaiwombole izigulitsidwa pa mtengo womwe unaikidwa.
27 Koma ngati ndi nyama yodetsedwa ndipo waiwombola mogwirizana ndi mtengo womwe unaikidwa, azipereka mtengo wa nyamayo nʼkuwonjezerapo limodzi mwa magawo 5 a mtengowo.+ Koma ngati sangaiwombole izigulitsidwa pa mtengo womwe unaikidwa.