Numeri 3:33 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 33 Mabanja a Amali ndi Amusi anachokera mwa Merari. Amenewa ndi amene anali mabanja a Amerari.+