-
Numeri 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Zinthu zopatulika za munthu aliyense zizikhala zake. Chilichonse chimene munthu angapereke kwa wansembe, chizikhala cha wansembeyo.’”
-