-
Numeri 5:10Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
10 Zinthu zopatulika zimene munthu aliyense azipereka, zizikhala za wansembe. Chilichonse chimene munthu angapereke kwa wansembe, chimenecho chizikhala chake.’”
-