-
Numeri 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 anabweretsa zopereka zawo pamaso pa Yehova. Zoperekazo zinali ngolo 6 zotseka pamwamba ndi ngʼombe zamphongo 12. Atsogoleri awiri anapereka ngolo imodzi, ndipo mtsogoleri aliyense anapereka ngʼombe yamphongo imodzi. Zoperekazo anafika nazo pachihema.
-