-
Numeri 7:3Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
3 Anabweretsa zopereka zawo pamaso pa Yehova. Zoperekazo zinali ngolo 6 zotseka pamwamba, ndi ng’ombe 12. Zimenezi zikutanthauza kuti atsogoleri awiri anapereka ngolo imodzi, ndipo mtsogoleri aliyense anapereka ng’ombe yamphongo imodzi. Zoperekazo anafika nazo pachihema chopatulika.
-