-
Numeri 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Ulandire zinthu zimenezi kwa iwo kuti zigwiritsidwe ntchito pa utumiki wapachihema chokumanako. Uzipereke kwa Alevi ndipo aliyense umupatse mogwirizana ndi zimene zikufunika pa ntchito yake.”
-