-
Numeri 7:5Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
-
-
5 “Ulandire zimenezi kwa iwo kuti zikhale zogwiritsa ntchito pa utumiki wa pachihema chokumanako. Uzipereke kwa Alevi, aliyense malinga ndi utumiki wake.”
-