Numeri 7:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Iye anapereka ngʼombe ziwiri, nkhosa 5 zamphongo, mbuzi 5 zamphongo, ndi ana a nkhosa 5 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yamgwirizano.+ Izi nʼzimene Abidana,+ mwana wa Gidiyoni anapereka.
65 Iye anapereka ngʼombe ziwiri, nkhosa 5 zamphongo, mbuzi 5 zamphongo, ndi ana a nkhosa 5 amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi kuti zikhale za nsembe yamgwirizano.+ Izi nʼzimene Abidana,+ mwana wa Gidiyoni anapereka.