Numeri 7:65 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 65 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Abidana mwana wa Gidoni.+
65 Ndipo za nsembe yachiyanjano,+ iye anapereka ng’ombe ziwiri, nkhosa zisanu zamphongo, mbuzi zisanu zamphongo, ndi ana a nkhosa asanu amphongo, aliyense wosapitirira chaka chimodzi. Izi n’zimene anapereka Abidana mwana wa Gidoni.+