Numeri 7:85 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Mbale yaikulu iliyonse yasiliva inali yolemera masekeli 130, ndipo mbale yolowa iliyonse inali yolemera masekeli 70. Siliva yense wa ziwiya zonsezi anali wolemera masekeli 2,400, mogwirizana ndi muyezo wa sekeli lakumalo oyera.+
85 Mbale yaikulu iliyonse yasiliva inali yolemera masekeli 130, ndipo mbale yolowa iliyonse inali yolemera masekeli 70. Siliva yense wa ziwiya zonsezi anali wolemera masekeli 2,400, mogwirizana ndi muyezo wa sekeli lakumalo oyera.+