Numeri 7:85 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 85 Mbale yaikulu iliyonse yasiliva inali yolemera masekeli 130, ndipo mbale yolowa iliyonse inali yolemera masekeli 70. Siliva yense wa ziwiya zonsezi anali wolemera masekeli 2,400, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera.+
85 Mbale yaikulu iliyonse yasiliva inali yolemera masekeli 130, ndipo mbale yolowa iliyonse inali yolemera masekeli 70. Siliva yense wa ziwiya zonsezi anali wolemera masekeli 2,400, malinga ndi muyezo wa sekeli la kumalo oyera.+