Ekisodo 30:13 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 13 Owerengedwa onse ayenera kupereka zotsatirazi: hafu ya sekeli yolingana ndi sekeli la kumalo oyera.*+ Magera* 20 amakwana sekeli limodzi. Hafu ya sekeli ndi chopereka kwa Yehova.+ Levitiko 27:25 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 25 “‘Mtengo woikidwiratu uliwonse uzikhala wolingana ndi sekeli la kumalo oyera. Sekeli limodzi lizikwana magera* 20.+
13 Owerengedwa onse ayenera kupereka zotsatirazi: hafu ya sekeli yolingana ndi sekeli la kumalo oyera.*+ Magera* 20 amakwana sekeli limodzi. Hafu ya sekeli ndi chopereka kwa Yehova.+
25 “‘Mtengo woikidwiratu uliwonse uzikhala wolingana ndi sekeli la kumalo oyera. Sekeli limodzi lizikwana magera* 20.+