Watchtower LAIBULALE YA PA INTANETI
Watchtower
LAIBULALE YA PA INTANETI
Chichewa
  • BAIBULO
  • MABUKU
  • MISONKHANO
  • 2 Mbiri 24:9
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 9 Atatero anauza anthu onse a ku Yuda ndi ku Yerusalemu kuti abweretse kwa Yehova msonkho wopatulika+ umene Mose+ mtumiki wa Mulungu woona analamula Aisiraeli m’chipululu.

  • Nehemiya 10:32
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 32 Kuwonjezera apo, tinadziikira malamulo akuti chaka chilichonse aliyense wa ife azipereka gawo limodzi mwa magawo atatu a sekeli kuti ndalama zimenezo akazigwiritsire ntchito pa utumiki wa panyumba ya Mulungu wathu.+

  • Mateyu 17:24
    Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika
    • 24 Atafika ku Kaperenao, anthu okhometsa msonkho wa madalakima awiri anafikira Petulo ndi kumufunsa kuti: “Kodi mphunzitsi wanu amapereka madalakima awiri a msonkho?”+

Mabuku a Chichewa (1974-2025)
Tulukani
Lowani
  • Chichewa
  • Tumizirani Ena
  • Zimene Mumakonda
  • Copyright © 2025 Watch Tower Bible and Tract Society of Pennsylvania
  • Zoyenera Kutsatira
  • Nkhani Yosunga Chinsinsi
  • Privacy Settings
  • JW.ORG
  • Lowani
Tumizirani Ena