Numeri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 Kenako Aleviwo aziika manja awo pamitu ya ngʼombe zamphongozo.+ Pambuyo pake, upereke kwa Yehova ngʼombe imodzi monga nsembe yamachimo, ndipo inayo uipereke monga nsembe yopsereza yophimbira machimo+ a Alevi.
12 Kenako Aleviwo aziika manja awo pamitu ya ngʼombe zamphongozo.+ Pambuyo pake, upereke kwa Yehova ngʼombe imodzi monga nsembe yamachimo, ndipo inayo uipereke monga nsembe yopsereza yophimbira machimo+ a Alevi.