Numeri 8:12 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 12 “Aleviwo aike manja awo pamitu ya ng’ombe zamphongozo.+ Pambuyo pake, upereke kwa Yehova ng’ombe imodzi monga nsembe yamachimo, ndipo inayo uipereke monga nsembe yopsereza yophimbira machimo+ a Alevi.
12 “Aleviwo aike manja awo pamitu ya ng’ombe zamphongozo.+ Pambuyo pake, upereke kwa Yehova ng’ombe imodzi monga nsembe yamachimo, ndipo inayo uipereke monga nsembe yopsereza yophimbira machimo+ a Alevi.