Numeri 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anakonza nsembe ya Pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba, madzulo kuli kachisisira,* mʼchipululu cha Sinai. Aisiraeliwo anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.
5 Iwo anakonza nsembe ya Pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba, madzulo kuli kachisisira,* mʼchipululu cha Sinai. Aisiraeliwo anachita zonse mogwirizana ndi zimene Yehova analamula Mose.