Numeri 9:5 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 5 Iwo anakonza nsembe ya pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba, madzulo kuli kachisisira, m’chipululu cha Sinai. Ana a Isiraeliwo anachita zonse malinga ndi zimene Yehova analamula Mose.+
5 Iwo anakonza nsembe ya pasika pa tsiku la 14 la mwezi woyamba, madzulo kuli kachisisira, m’chipululu cha Sinai. Ana a Isiraeliwo anachita zonse malinga ndi zimene Yehova analamula Mose.+