Numeri 10:9 Baibulo la Dziko Latsopano la Malemba Opatulika 9 Ngati mukufunika kumenya nkhondo mʼdziko lanu polimbana ndi mdani amene akukuzunzani, muziliza malipengawo+ posonyeza kuti mukuitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Yehova Mulungu wanu adzakukumbukirani ndipo adzakupulumutsani kwa adani anuwo.
9 Ngati mukufunika kumenya nkhondo mʼdziko lanu polimbana ndi mdani amene akukuzunzani, muziliza malipengawo+ posonyeza kuti mukuitanira asilikali kunkhondo. Mukatero, Yehova Mulungu wanu adzakukumbukirani ndipo adzakupulumutsani kwa adani anuwo.